Maliro 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova wandichotsera anthu anga onse amphamvu nʼkuwakankhira pambali.+ Wandiitanitsira msonkhano kuti aphwanye anyamata anga.+ Yehova wapondaponda namwali, mwana wamkazi wa Yuda, moponderamo mphesa.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:15 Nsanja ya Olonda,6/1/2007, tsa. 89/1/1988, ptsa. 26-27
15 Yehova wandichotsera anthu anga onse amphamvu nʼkuwakankhira pambali.+ Wandiitanitsira msonkhano kuti aphwanye anyamata anga.+ Yehova wapondaponda namwali, mwana wamkazi wa Yuda, moponderamo mphesa.+