Maliro 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikulira chifukwa cha zinthu zimenezi.+ Misozi ikutuluka mʼmaso mwanga. Chifukwa aliyense amene akananditonthoza kapena kunditsitsimula, ali kutali ndi ine. Ana anga awonongedwa ndipo mdani wanga wapambana.
16 Ndikulira chifukwa cha zinthu zimenezi.+ Misozi ikutuluka mʼmaso mwanga. Chifukwa aliyense amene akananditonthoza kapena kunditsitsimula, ali kutali ndi ine. Ana anga awonongedwa ndipo mdani wanga wapambana.