Maliro 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ziyoni watambasula manja ake.+ Palibe aliyense woti amutonthoze. Yehova walamula adani onse a Yakobo amene amuzungulira kuti amuukire.+ Yerusalemu wakhala chinthu chonyansa kwa iwo.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:17 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 26
17 Ziyoni watambasula manja ake.+ Palibe aliyense woti amutonthoze. Yehova walamula adani onse a Yakobo amene amuzungulira kuti amuukire.+ Yerusalemu wakhala chinthu chonyansa kwa iwo.+