Maliro 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndaitana anthu amene ankandikonda, koma anthuwo andichitira zachinyengo.+ Ansembe anga ndiponso akuluakulu atha mumzinda.Atha pamene amafunafuna chakudya choti adye kuti akhale ndi moyo.+
19 Ndaitana anthu amene ankandikonda, koma anthuwo andichitira zachinyengo.+ Ansembe anga ndiponso akuluakulu atha mumzinda.Atha pamene amafunafuna chakudya choti adye kuti akhale ndi moyo.+