Maliro 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuipa kwawo konse kuonekere pamaso panu ndipo muwalange koopsa,+Ngati mmene mwandilangira ine chifukwa cha zolakwa zanga zonse. Ndikuusa moyo kwambiri ndipo mtima wanga ukudwala.
22 Kuipa kwawo konse kuonekere pamaso panu ndipo muwalange koopsa,+Ngati mmene mwandilangira ine chifukwa cha zolakwa zanga zonse. Ndikuusa moyo kwambiri ndipo mtima wanga ukudwala.