Maliro 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wameza mopanda chifundo malo onse amene Yakobo ankakhala. Mokwiya kwambiri, iye wagwetsa mipanda yolimba kwambiri ya mwana wamkazi wa Yuda.+ Iye wagwetsera pansi komanso kuipitsa ufumu+ ndi akalonga ake.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 26
2 Yehova wameza mopanda chifundo malo onse amene Yakobo ankakhala. Mokwiya kwambiri, iye wagwetsa mipanda yolimba kwambiri ya mwana wamkazi wa Yuda.+ Iye wagwetsera pansi komanso kuipitsa ufumu+ ndi akalonga ake.+