Maliro 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wakunga* uta wake ngati mdani. Wakweza dzanja lake lamanja kuti atiukire ngati ndife adani ake.+Iye anapitiriza kupha anthu onse ofunika kwambiri.+ Anakhuthulira ukali wake ngati moto+ mutenti ya mwana wamkazi wa Ziyoni.+
4 Wakunga* uta wake ngati mdani. Wakweza dzanja lake lamanja kuti atiukire ngati ndife adani ake.+Iye anapitiriza kupha anthu onse ofunika kwambiri.+ Anakhuthulira ukali wake ngati moto+ mutenti ya mwana wamkazi wa Ziyoni.+