-
Maliro 2:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Iye wameza nsanja zonse za Isiraeli.
Wawononga malo ake onse okhala ndi mipanda yolimba kwambiri.
Ndipo wachititsa kuti paliponse pakhale maliro komanso kulira mumzinda wa mwana wamkazi wa Yuda.
-