Maliro 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye wapasula msasa wake+ ngati chisimba chamʼmunda. Iye wathetsa zikondwerero zake.+ Yehova wachititsa kuti zikondwerero ndi sabata ziiwalike mu Ziyoni,Ndipo chifukwa cha mkwiyo wake waukulu sakuganiziranso za mfumu ndi wansembe.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Nsanja ya Olonda,6/1/2007, tsa. 99/1/1988, ptsa. 26-27
6 Iye wapasula msasa wake+ ngati chisimba chamʼmunda. Iye wathetsa zikondwerero zake.+ Yehova wachititsa kuti zikondwerero ndi sabata ziiwalike mu Ziyoni,Ndipo chifukwa cha mkwiyo wake waukulu sakuganiziranso za mfumu ndi wansembe.+