Maliro 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova wakana guwa lake lansembe.Iye wasiya malo ake opatulika.+ Wapereka mʼmanja mwa adani makoma a nsanja zake zotetezeka.+ Adaniwo afuula mʼnyumba ya Yehova+ ngati pa tsiku lachikondwerero.
7 Yehova wakana guwa lake lansembe.Iye wasiya malo ake opatulika.+ Wapereka mʼmanja mwa adani makoma a nsanja zake zotetezeka.+ Adaniwo afuula mʼnyumba ya Yehova+ ngati pa tsiku lachikondwerero.