Maliro 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mageti ake amira munthaka.+ Wawononga ndi kuthyolathyola mipiringidzo yake. Mfumu yake ndi akalonga ake ali pakati pa anthu a mitundu ina.+ Anthu sakutsatira malamulo.* Ndipo ngakhale aneneri ake sakuona masomphenya ochokera kwa Yehova.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:9 Yeremiya, tsa. 73
9 Mageti ake amira munthaka.+ Wawononga ndi kuthyolathyola mipiringidzo yake. Mfumu yake ndi akalonga ake ali pakati pa anthu a mitundu ina.+ Anthu sakutsatira malamulo.* Ndipo ngakhale aneneri ake sakuona masomphenya ochokera kwa Yehova.+