Maliro 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akuluakulu a mwana wamkazi wa Ziyoni akhala pansi ndipo akhala chete.+ Iwo athira fumbi pamitu yawo ndipo avala ziguduli.+ Anamwali a ku Yerusalemu aweramitsa mitu yawo mpaka pansi.
10 Akuluakulu a mwana wamkazi wa Ziyoni akhala pansi ndipo akhala chete.+ Iwo athira fumbi pamitu yawo ndipo avala ziguduli.+ Anamwali a ku Yerusalemu aweramitsa mitu yawo mpaka pansi.