Maliro 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maso anga atopa ndi kugwetsa misozi.+ Mʼmimba mwanga mukubwadamuka. Chiwindi changa chakhuthulidwa pansi chifukwa cha kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga,+Ndiponso chifukwa chakuti ana ndi makanda akukomoka mʼmabwalo a mzinda.+
11 Maso anga atopa ndi kugwetsa misozi.+ Mʼmimba mwanga mukubwadamuka. Chiwindi changa chakhuthulidwa pansi chifukwa cha kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga,+Ndiponso chifukwa chakuti ana ndi makanda akukomoka mʼmabwalo a mzinda.+