Maliro 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Masomphenya amene aneneri anu anaona ndi abodza komanso achabechabe,+Ndipo sanaulule zolakwa zanu nʼcholinga choti musatengedwe kupita ku ukapolo,+Koma ankaona masomphenya abodza komanso okusocheretsani.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 26
14 Masomphenya amene aneneri anu anaona ndi abodza komanso achabechabe,+Ndipo sanaulule zolakwa zanu nʼcholinga choti musatengedwe kupita ku ukapolo,+Koma ankaona masomphenya abodza komanso okusocheretsani.+