Maliro 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adani ako onse atsegula pakamwa pawo. Akuimba mluzu ndi kukukuta mano nʼkumanena kuti: “Ameneyu tamumeza.+ Lero ndi tsiku limene takhala tikuliyembekezera.+ Lafika ndipo taliona!”+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Nsanja ya Olonda,6/1/2007, tsa. 9
16 Adani ako onse atsegula pakamwa pawo. Akuimba mluzu ndi kukukuta mano nʼkumanena kuti: “Ameneyu tamumeza.+ Lero ndi tsiku limene takhala tikuliyembekezera.+ Lafika ndipo taliona!”+