Maliro 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova wachita zimene ankafuna.+ Wakwaniritsa zimene ananena,+Zimene analamula kalekale.+ Wakuwononga mopanda chisoni.+ Wachititsa kuti adani ako asangalale chifukwa cha zimene zakuchitikira. Wawonjezera mphamvu* za adani ako. Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Yeremiya, tsa. 154 Nsanja ya Olonda,6/1/2007, tsa. 9
17 Yehova wachita zimene ankafuna.+ Wakwaniritsa zimene ananena,+Zimene analamula kalekale.+ Wakuwononga mopanda chisoni.+ Wachititsa kuti adani ako asangalale chifukwa cha zimene zakuchitikira. Wawonjezera mphamvu* za adani ako.