Maliro 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu akulirira Yehova ndi mtima wawo wonse, iwe mpanda wa mwana wamkazi wa Ziyoni. Misozi iyende ngati mtsinje masana ndi usiku. Usapume ndipo diso* lako lisasiye kulira.
18 Anthu akulirira Yehova ndi mtima wawo wonse, iwe mpanda wa mwana wamkazi wa Ziyoni. Misozi iyende ngati mtsinje masana ndi usiku. Usapume ndipo diso* lako lisasiye kulira.