Maliro 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nyamuka! Lira mofuula usiku, pa nthawi yoyamba ulonda. Khuthula mtima wako pamaso pa Yehova ngati madzi. Pemphera utakweza manja ako kwa iye chifukwa cha ana ako,Amene akukomoka ndi njala pamphambano za misewu yonse.+
19 Nyamuka! Lira mofuula usiku, pa nthawi yoyamba ulonda. Khuthula mtima wako pamaso pa Yehova ngati madzi. Pemphera utakweza manja ako kwa iye chifukwa cha ana ako,Amene akukomoka ndi njala pamphambano za misewu yonse.+