Maliro 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munaitana zoopsa kuchokera kumbali zonse ngati kuti mukuitana anthu pa tsiku lachikondwerero.+ Pa tsiku la mkwiyo wa Yehova panalibe aliyense amene anathawa kapena kupulumuka.+Ana onse amene ndinabereka komanso kuwalera, mdani wanga anawapha.+
22 Munaitana zoopsa kuchokera kumbali zonse ngati kuti mukuitana anthu pa tsiku lachikondwerero.+ Pa tsiku la mkwiyo wa Yehova panalibe aliyense amene anathawa kapena kupulumuka.+Ana onse amene ndinabereka komanso kuwalera, mdani wanga anawapha.+