Maliro 3:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Tiyeni tifufuze ndi kuganizira mozama makhalidwe athu+ ndipo tibwerere kwa Yehova.+