Maliro 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Golide amene anali wowala komanso woyengedwa bwino,+ sakuwalanso. Miyala yopatulika+ yamwazika pamphambano zonse za misewu.+
4 Golide amene anali wowala komanso woyengedwa bwino,+ sakuwalanso. Miyala yopatulika+ yamwazika pamphambano zonse za misewu.+