Maliro 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chilango chimene mwana wamkazi wa anthu anga walandira nʼchachikulu kuposa chimene mzinda wa Sodomu unalandira chifukwa cha machimo ake.+Mzinda umenewu unawonongedwa mʼkanthawi kochepa, ndipo panalibe dzanja limene linauthandiza.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Yeremiya, ptsa. 107-108
6 Chilango chimene mwana wamkazi wa anthu anga walandira nʼchachikulu kuposa chimene mzinda wa Sodomu unalandira chifukwa cha machimo ake.+Mzinda umenewu unawonongedwa mʼkanthawi kochepa, ndipo panalibe dzanja limene linauthandiza.+