Maliro 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anaziri ake+ anali oyera kwambiri, anali oyera kuposa mkaka. Anali ofiira kuposa miyala yamtengo wapatali ya korali. Anali onyezimira ngati miyala ya safiro.
7 Anaziri ake+ anali oyera kwambiri, anali oyera kuposa mkaka. Anali ofiira kuposa miyala yamtengo wapatali ya korali. Anali onyezimira ngati miyala ya safiro.