Maliro 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene anaphedwa ndi lupanga aliko bwino kusiyana ndi amene anafa ndi njala.+Amenewa anafooka nʼkufa chifukwa chosowa chakudya ndipo anafa ngati abayidwa ndi lupanga.
9 Amene anaphedwa ndi lupanga aliko bwino kusiyana ndi amene anafa ndi njala.+Amenewa anafooka nʼkufa chifukwa chosowa chakudya ndipo anafa ngati abayidwa ndi lupanga.