Maliro 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Azimayi amene amakhala achifundo, aphika ana awo ndi manja awo.+ Anawo akhala chakudya chawo pa nthawi yachisoni pamene mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+ Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:10 Yeremiya, ptsa. 154-155 Nsanja ya Olonda,8/1/1989, tsa. 29
10 Azimayi amene amakhala achifundo, aphika ana awo ndi manja awo.+ Anawo akhala chakudya chawo pa nthawi yachisoni pamene mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+