Maliro 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngakhale panopa maso athu afooka chifukwa choyembekezera thandizo lomwe silikubwera.+ Tinafufuza thandizo ku mtundu wa anthu umene sukanatha kutipulumutsa.+
17 Ngakhale panopa maso athu afooka chifukwa choyembekezera thandizo lomwe silikubwera.+ Tinafufuza thandizo ku mtundu wa anthu umene sukanatha kutipulumutsa.+