Maliro 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akutisakasaka kulikonse kumene tikupita,+ moti sitingathenso kuyenda mʼmabwalo a mizinda yathu. Mapeto a moyo wathu ayandikira. Masiku athu atha chifukwa mapeto a moyo wathu afika.
18 Akutisakasaka kulikonse kumene tikupita,+ moti sitingathenso kuyenda mʼmabwalo a mizinda yathu. Mapeto a moyo wathu ayandikira. Masiku athu atha chifukwa mapeto a moyo wathu afika.