Maliro 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu amene ankatithamangitsa anali aliwiro kuposa ziwombankhanga zouluka mʼmwamba.+ Iwo anatithamangitsa mʼmapiri. Anatibisalira mʼchipululu. Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:19 Nsanja ya Olonda,6/15/1996, ptsa. 9-10
19 Anthu amene ankatithamangitsa anali aliwiro kuposa ziwombankhanga zouluka mʼmwamba.+ Iwo anatithamangitsa mʼmapiri. Anatibisalira mʼchipululu.