Maliro 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Wodzozedwa wa Yehova,+ amene ndi mpweya wotuluka mumphuno mwathu, wagwidwa mʼdzenje lawo lalikulu.+Ponena za ameneyu, ife tinkanena kuti: “Tidzakhala mumthunzi wake pakati pa mitundu ya anthu.” Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:20 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 27
20 Wodzozedwa wa Yehova,+ amene ndi mpweya wotuluka mumphuno mwathu, wagwidwa mʼdzenje lawo lalikulu.+Ponena za ameneyu, ife tinkanena kuti: “Tidzakhala mumthunzi wake pakati pa mitundu ya anthu.”