Maliro 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kondwa ndipo usangalale, iwe mwana wamkazi wa Edomu,+ amene ukukhala mʼdziko la Uzi. Koma iwenso kapu ya tsoka idzakupeza.+ Udzaledzera ndipo udzavula nʼkukhala maliseche.+
21 Kondwa ndipo usangalale, iwe mwana wamkazi wa Edomu,+ amene ukukhala mʼdziko la Uzi. Koma iwenso kapu ya tsoka idzakupeza.+ Udzaledzera ndipo udzavula nʼkukhala maliseche.+