Ezekieli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mʼchaka cha 30, mʼmwezi wa 4, pa tsiku la 5 la mweziwo, pamene ndinali pakati pa anthu amene anali ku ukapolo+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara,+ kumwamba kunatseguka ndipo ndinayamba kuona masomphenya a Mulungu. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Nsanja ya Olonda,6/15/1998, tsa. 159/15/1988, tsa. 11
1 Mʼchaka cha 30, mʼmwezi wa 4, pa tsiku la 5 la mweziwo, pamene ndinali pakati pa anthu amene anali ku ukapolo+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara,+ kumwamba kunatseguka ndipo ndinayamba kuona masomphenya a Mulungu.