Ezekieli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinaona mphepo yamkuntho+ ikuchokera kumpoto. Ndinaonanso mtambo waukulu komanso moto walawilawi*+ utazunguliridwa ndi kuwala. Pakati pa motowo panali chinachake chooneka ngati siliva wosakanikirana ndi golide.+
4 Ndinaona mphepo yamkuntho+ ikuchokera kumpoto. Ndinaonanso mtambo waukulu komanso moto walawilawi*+ utazunguliridwa ndi kuwala. Pakati pa motowo panali chinachake chooneka ngati siliva wosakanikirana ndi golide.+