Ezekieli 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Umu ndi mmene nkhope zawo zinalili. Mapiko awo anali otambasukira mʼmwamba. Mngelo aliyense anali ndi mapiko awiri ogundana, ndipo mapiko ena awiri ankaphimba matupi awo.+
11 Umu ndi mmene nkhope zawo zinalili. Mapiko awo anali otambasukira mʼmwamba. Mngelo aliyense anali ndi mapiko awiri ogundana, ndipo mapiko ena awiri ankaphimba matupi awo.+