Ezekieli 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawilowo ankawala ngati mwala wa kulusolito, ndipo mawilo 4 onsewo ankaoneka mofanana. Anapangidwa mooneka ngati wilo lina lili pakati pa linzake.* Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Nsanja ya Olonda,3/15/1991, tsa. 9
16 Mawilowo ankawala ngati mwala wa kulusolito, ndipo mawilo 4 onsewo ankaoneka mofanana. Anapangidwa mooneka ngati wilo lina lili pakati pa linzake.*