Ezekieli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Angelo aja akamayenda, nawonso mawilowo ankayenda nawo limodzi. Angelowo akamakwera mʼmwamba kuchokera pansi, mawilowonso ankakwera mʼmwamba.+
19 Angelo aja akamayenda, nawonso mawilowo ankayenda nawo limodzi. Angelowo akamakwera mʼmwamba kuchokera pansi, mawilowonso ankakwera mʼmwamba.+