-
Ezekieli 1:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Angelowo akamayenda, mawilowonso ankayenda. Angelowo akaima, mawilowonso ankaima. Angelowo akakwera mʼmwamba kuchokera pansi, mawilowonso ankakwera mʼmwamba chifukwa mzimu womwe unkatsogolera angelowo unkatsogoleranso mawilowo.
-