Ezekieli 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamwamba pa mitu ya angelowo panali chinachake chooneka ngati thambo chimene chinayalidwa pamwamba pa mitu yawo. Chinthucho chinali chonyezimira ngati madzi oundana ochititsa chidwi.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:22 Nsanja ya Olonda,3/15/1991, tsa. 10
22 Pamwamba pa mitu ya angelowo panali chinachake chooneka ngati thambo chimene chinayalidwa pamwamba pa mitu yawo. Chinthucho chinali chonyezimira ngati madzi oundana ochititsa chidwi.+