-
Ezekieli 1:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mapiko a angelo omwe anali pansi pa chinthu chooneka ngati thambocho, anali otambasukira mʼmwamba ndipo phiko lililonse linkagundana ndi linzake. Mngelo aliyense anali ndi mapiko awiri amene ankaphimba mbali imodzi ya thupi lake, ndipo mapiko ena awiri ankaphimba mbali ina yotsalayo.
-