-
Ezekieli 1:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Pamwamba pa chinthu chooneka ngati thambo chimene chinali pamwamba pa mitu yawo pankamveka mawu. (Akaima, ankatsitsa mapiko awo pansi.)
-