Ezekieli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu,* imirira kuti ndikulankhule.”+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 11