Ezekieli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikukutumiza kwa ana osamvera komanso ouma mtima+ ndipo ukawauze kuti, ‘Izi nʼzimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena.’ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, ptsa. 2-3
4 Ndikukutumiza kwa ana osamvera komanso ouma mtima+ ndipo ukawauze kuti, ‘Izi nʼzimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena.’