Ezekieli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kaya akamvetsera kapena ayi, popeza iwo ndi anthu opanduka,+ adzadziwabe ndithu kuti pakati pawo panali mneneri.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:5 Nsanja ya Olonda,7/15/2008, tsa. 115/1/1997, tsa. 23
5 Kaya akamvetsera kapena ayi, popeza iwo ndi anthu opanduka,+ adzadziwabe ndithu kuti pakati pawo panali mneneri.+