Ezekieli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iwe mwana wa munthu, mvetsera zimene ndikukuuza. Usapanduke ngati anthu opandukawa. Tsegula pakamwa pako kuti udye zimene ndikukupatsa.”+
8 Koma iwe mwana wa munthu, mvetsera zimene ndikukuuza. Usapanduke ngati anthu opandukawa. Tsegula pakamwa pako kuti udye zimene ndikukupatsa.”+