Ezekieli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, idya chimene chili pamaso pakochi.* Idya mpukutu uwu ndipo upite kukalankhula ndi nyumba ya Isiraeli.”+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, tsa. 6 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,6/2017, tsa. 5
3 Kenako anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, idya chimene chili pamaso pakochi.* Idya mpukutu uwu ndipo upite kukalankhula ndi nyumba ya Isiraeli.”+
3:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, tsa. 6 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,6/2017, tsa. 5