Ezekieli 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sindikukutuma kwa mitundu yambiri ya anthu amene amalankhula chilankhulo chovuta kumva kapena chilankhulo chimene sukuchidziwa, amene sungathe kumvetsetsa zimene akunena. Ndikanakhala kuti ndakutumiza kwa anthu amenewo, akanakumvera.+
6 Sindikukutuma kwa mitundu yambiri ya anthu amene amalankhula chilankhulo chovuta kumva kapena chilankhulo chimene sukuchidziwa, amene sungathe kumvetsetsa zimene akunena. Ndikanakhala kuti ndakutumiza kwa anthu amenewo, akanakumvera.+