Ezekieli 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma a nyumba ya Isiraeli akakana kukumvera, chifukwa iwo sakufuna kundimvera.+ Anthu onse a nyumba ya Isiraeli ndi amakani komanso osamva.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:7 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, ptsa. 3-4
7 Koma a nyumba ya Isiraeli akakana kukumvera, chifukwa iwo sakufuna kundimvera.+ Anthu onse a nyumba ya Isiraeli ndi amakani komanso osamva.+