Ezekieli 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndachititsa kuti chipumi chako chikhale ngati mwala wa dayamondi, cholimba kuposa mwala wa nsangalabwi.+ Usawaope kapena kuchita mantha ndi nkhope zawo,+ chifukwa iwo ndi anthu opanduka.” Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,11/1/1991, tsa. 317/15/1988, tsa. 30
9 Ndachititsa kuti chipumi chako chikhale ngati mwala wa dayamondi, cholimba kuposa mwala wa nsangalabwi.+ Usawaope kapena kuchita mantha ndi nkhope zawo,+ chifukwa iwo ndi anthu opanduka.”
3:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,11/1/1991, tsa. 317/15/1988, tsa. 30