Ezekieli 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pita pakati pa anthu a mtundu wako* amene anatengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo ukalankhule nawo. Ukawauze kuti, ‘Izi nʼzimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa wanena,’ kaya akamvetsera kapena ayi.”+
11 Pita pakati pa anthu a mtundu wako* amene anatengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo ukalankhule nawo. Ukawauze kuti, ‘Izi nʼzimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa wanena,’ kaya akamvetsera kapena ayi.”+