Ezekieli 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho ndinapita kwa anthu amene anatengedwa kupita ku ukapolo omwe anali ku Tele-abibu. Anthuwa ankakhala pafupi ndi mtsinje wa Kebara.+ Ndinakhala nawo kumeneko masiku 7 nditasokonezeka maganizo.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, ptsa. 4-5 Nsanja ya Olonda,7/1/2007, tsa. 139/15/1988, tsa. 12
15 Choncho ndinapita kwa anthu amene anatengedwa kupita ku ukapolo omwe anali ku Tele-abibu. Anthuwa ankakhala pafupi ndi mtsinje wa Kebara.+ Ndinakhala nawo kumeneko masiku 7 nditasokonezeka maganizo.+
3:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, ptsa. 4-5 Nsanja ya Olonda,7/1/2007, tsa. 139/15/1988, tsa. 12