Ezekieli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Iwe mwana wa munthu, ine ndakuika kuti ukhale mlonda wa nyumba ya Isiraeli.+ Choncho ukamva mawu ochokera pakamwa panga ukuyenera kuwachenjeza.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:17 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, ptsa. 10, 12
17 “Iwe mwana wa munthu, ine ndakuika kuti ukhale mlonda wa nyumba ya Isiraeli.+ Choncho ukamva mawu ochokera pakamwa panga ukuyenera kuwachenjeza.+